Lonkyz ,photocopy and printing machine

Lonkyz ,photocopy and printing machine Lonkyz mwβœŠπŸŽ…

Mzimu oyela kumuikila malile πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”
06/12/2024

Mzimu oyela kumuikila malile πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”πŸ€”




Mtsogoleri wa mpingo wa Katolika pa dziko lonse, Papa Francis, walimbikitsa alaliki kuti ulaliki wawo usamatalike kupitilira mphindi khumi.

Poyankhula Lachitatu sabata ino pa tchalitchi cha Saint Peter's Square ku Rome, Papa Francis wati nthawi zonse ulaliki umayenera kutsogozedwa ndi Mzimu Woyera, choncho kulalikira nthawi yaitali kumamuika mlalikiyo pa mayesero olalikira za m'mutu mwake osati zomwe Mzimu Woyera akunena.

Malingana ndi tsamba la Vatican News, Papa Francis wati uthenga wabwino uyenera kulalikidwa β€œmwa Mzimu Woyera. Kulalikira ndi kudzoza kwa Mzimu Woyera kumatanthauza kufalitsa, pamodzi ndi malingaliro ndi chiphunzitso, moyo ndi kukhudzika kwakukulu, ndipo motero osati ndi mawu a nzeru okopa, koma ndi chionetsero cha Mzimu ndi mphamvu."

Popitilira, Papa Francis wati, β€œPakadutsa mphindi 8, kulalikira kumabalalika ndipo palibe amene amakumvetsa. Musapitirire mphindi 10, ayi! Izi ndizofunikira kwambiri."

Iye anati, alaliki ayenera kupempherera chisomo cha Mzimu Woyera kuti alengeze Khristu m’kulalikira kwawo. Apa anatsindikaso kuti alaliki sayenera kudzilalikira okha koma Yesu Mkhilisitu.

Pakadali pano, mtsutso wakula pamasamba anchezo. Pomwe ena akugwirizana ndi zomwe Papa Francis wayankhulazi, ena akutsutsa ponena kuti Mzimu Woyera sumayenera kudulilidwa malire.

21/08/2024

Good night 🌚

18/08/2024

HbD Gun boss

17/08/2024

Onesmus remix ndi joa boy now is outπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™ŒπŸ™Œ

Congratulations to the International Pangolin, Onesimus as a he won as Best male artist at the 8th Annual HAPA AWARDS la...
11/08/2024

Congratulations to the International Pangolin, Onesimus as a he won as Best male artist at the 8th Annual HAPA AWARDS lastnight in Tanzania πŸ‡ΉπŸ‡Ώ uku kunali achina Hamornizer, Raivany, Khalid and kcee komawathuyu sanagawe kamba

09/08/2024

With Joeboy – I just got recognized as one of their top fans!

30/07/2024

With Kell Kay – I just got recognized as one of their top fans!

30/07/2024

With Kell Kay – I just got recognized as one of their top fans!kelz am proud

27/05/2024

Let's keep faith

Address

Area 25
Capital Hill
GB

Telephone

+265992170748

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lonkyz ,photocopy and printing machine posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share