Chisomo TV

Chisomo TV Chisomo TV:

Bungwe logawa madzi la Lilongwe Water Board (LWB) latsutsa mphekesera zomwe zikufala pa masamba a mchezo kuti lakweza mt...
20/01/2026

Bungwe logawa madzi la Lilongwe Water Board (LWB) latsutsa mphekesera zomwe zikufala pa masamba a mchezo kuti lakweza mtengo wa madzi.

Kudzera pa tsamba lake la facebook, LWB yati chikalata chomwe chikuzungulirachi ndi chabodza.


Bungwe la ESCOM lakweza mtengo wa magetsi ndi 12%, izi ndi malinga chikalata chomwe bungweli latulutsa.Bungweli latiso k...
20/01/2026

Bungwe la ESCOM lakweza mtengo wa magetsi ndi 12%, izi ndi malinga chikalata chomwe bungweli latulutsa.

Bungweli latiso kukwera mtengoku kuthandiziraso kuti ESCOM izichita machawi pokonza mavuto okhudza magetsi.


 Malawi Energy Regulatory Authority has with immediate effect adjusted upward the pump price for petrol and diesel. This...
20/01/2026



Malawi Energy Regulatory Authority has with immediate effect adjusted upward the pump price for petrol and diesel.

This is according to a statement signed by MERA's board chairperson Lucas Kondowe.

Petrol will now be selling at K4, 965 from K3, 499 representing 41.90% increase, while diesel will be selling at K4, 945 from K3, 500 representing 41.29% increase.


12/01/2026

Behind the scenes

We were there for the wedding of Grant and Beat today in Dedza district.
13/12/2025

We were there for the wedding of Grant and Beat today in Dedza district.


Address

Dedza

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chisomo TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chisomo TV:

Share