Grid&Beyond

Grid&Beyond Grid&Beyond offers innovative energy solutions aimed at improving energy access and sustainability.

Proud to renew our membership and join Renewable Energy Industries Association of Malawi in it’s movement to drive Malaw...
04/05/2026

Proud to renew our membership and join Renewable Energy Industries Association of Malawi in it’s movement to drive Malawi’s transition to a cleaner, greener and more sustainable future.

CLOSED!!
02/05/2026

CLOSED!!

Ana asasiye kuwerenga poti ESCOM yazimitsa magetsi, oyang’anira kumunda asamachite kuunikira phone komanso geni yanuyo o...
20/04/2026

Ana asasiye kuwerenga poti ESCOM yazimitsa magetsi, oyang’anira kumunda asamachite kuunikira phone komanso geni yanuyo osaika kendulo pamwamba………sankhani kukhala otsogola pounikira nyale ya Solar.

Timapezeka mu:
Kizito House
Area 47 sector 2
Pafupi ndi Assemblies of God Church!

LILONGWE - Omwe mumadikilira ma double Stove nthawi yanu yafika - we now have double stoves in stock. Ngati simukuyankhi...
18/04/2026

LILONGWE - Omwe mumadikilira ma double Stove nthawi yanu yafika - we now have double stoves in stock.

Ngati simukuyankhidwa phone ndi agent wakudera lanu, tilembereni ku inbox dzina lanu, komwe mukukhala ndi phone number yanu.

Note: Moni, Hello, Hie sitimayankha.

Happy cooking moments!

Onesetsani kuti munthu amene mukulankhula naye mukafuna kugula eCook stove amagwira ntchito ku company yovomerezeka……..n...
27/03/2026

Onesetsani kuti munthu amene mukulankhula naye mukafuna kugula eCook stove amagwira ntchito ku company yovomerezeka……..ngati mukukaikira funsani ku Grid&Beyond pa 0999176480 kapena ku Self Help Africa kudzera pa 4366 ndipo adzakuthandizani.

Musabetse ndalama zanu!

Zagwa mtengo! 4,000 kugula magetsi pheee!
23/03/2026

Zagwa mtengo! 4,000 kugula magetsi pheee!

Tikulengeza zakupezeka kwama SINGLE Stove kuno ku Grid&Beyond………yankhulani ndi agent wakudera kwanu kudzera pama numbers...
23/03/2026

Tikulengeza zakupezeka kwama SINGLE Stove kuno ku Grid&Beyond………yankhulani ndi agent wakudera kwanu kudzera pama numbers omwe ali pa flyer kuti mupeze yanu

Akasi tabweretsaso ma PICCO PLUS abwino kwa Ana omwe ali ma boarding schools MK25,000 yokha basi. Imbani pa 0992878782 k...
04/02/2026

Akasi tabweretsaso ma PICCO PLUS abwino kwa Ana omwe ali ma boarding schools MK25,000 yokha basi. Imbani pa 0992878782 kuti mudziwe zambiri

20/01/2026

Kuphika kwaphindu

Lilongwe and Blantyre siyani kuphikira makala, yambani kuphika mwaukhondo komanso mwachangu ndi induction stove iyi………40...
12/01/2026

Lilongwe and Blantyre siyani kuphikira makala, yambani kuphika mwaukhondo komanso mwachangu ndi induction stove iyi………40,000 mutenga Stove ndi mapoto awiri. T&Cs apply!

Lilongwe - Area 47 sector 2
Kizito House - near Assemblies of God Church
0992878782
0999176480
0981329844

Blantyre - Chileka pa 10 Miles
0984061166
099 500 1109

Agulireni anthu ku munda adziunikira……..19,500 only. Tikupezeka ku Lilongwe area 47 sector 2 in Kizito House pafupi ndi ...
12/01/2026

Agulireni anthu ku munda adziunikira……..19,500 only. Tikupezeka ku Lilongwe area 47 sector 2 in Kizito House pafupi ndi Assemblies of God Church

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Grid&Beyond posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share