09/03/2024
Nkhani yabwino kwa ma kasitomala athu nonse. Pofuna kukuthokozani, komanso poona ndi mmene Kwacha alili, tangotsitsiratu ndi 35% kuchoka pa mitengo ija.
Pambali potsutsa mitengo, pajatu mitengo yathu ndi ya ziiiiii... indetu wokambirana, cholinga chathu ndi kukumangirani zinthu zabwino zobweretsa chimwemwe ndi mtendere wa Mu Mtima.
Kaya kumanga:👇
1). Nyumba,
2). Mpanda,
3). Office,
4). School,
5). Church,
6). Malo ochitira za masewero,
Ndi zina zonse zokhuza kumanga, tipatseni ife ntchito kuti timange nyumba za maziko olimba, zokhalitsa, zopatsa kaso, zodalilika ndi zokomera inu eni.
Ngati mukufuna kumva zambiri, imbani phone pa manambala awa:
+265 888 878 678 / +265 990 135 224
+265 997 286 698 / +265 889 726 008
Kumanga kwaphweka, tili pa
, Machinjiri, Blantyre.
NNjuli BuildersBuilt on Quality Foundations