Lloyd kanyimbi

Lloyd kanyimbi Block production department ,construction department finishing department,P.O.P department and roofing department all at one place

19/09/2025

Chidyereni ndasi 2019 mmmmmmmmmmm

11/09/2025



Bungwe loona za ogula katundu la Consumers Association of Malawi (CAMA) lati zomwe President Lazarus Chakwera wakhala akunena kuti anthu ena akukweza dala mitengo ya katundu osiyanasiyana kuti iye ndi boma lake awoneke olephera, sizoona.

Mkulu wa bungweli, a John Kapito, wati anthu amene amuzungulira Pulezidenti Chakwera m'boma, kuphatikizapo alangizi, sakumuuza zoona.

"Pulezidenti akudziwa chimene chimachititsa kuti mitengo ya zinthu idzikwera ndi kutsika.
Anthu amene ali m'boma ndi nthambi zomwe ndi za boma adziwafotokozera a Pulezidenti zoona.

"Anthu amene ali m'boma amene amagula zinthu ndi amene apezerapo mwayi omayitanitsa katundu wa kunja koma pa mitengo yokwera kwambiri zimenezo akuchititsa ndi anthu amene ali m'boma kale chifukwa sungakhale ndi mphamvu zopanga mitengo ngati uli kunja kwa boma."

Pulezidenti Lazarus Chakwera wakhala akulankhula m'misonkhano yokopa anthu kuti anthu ena akukweza dala mitengo ya katundu osiyanasiyana kuti iye asadzapambane pa chisankho chikudzachi.

(by Alfred Guta-Nsanje:09/11/25)

11/09/2025

Kupatula Nkhuku Tembo ndi Green Mamba, ndinyama ina iti yomwe yilindi surname?😂🤣😂

ZOSATILA ZAYAMBA KUFIKA KUNO KU MAIN TALLY CENTER...1,2 ..1,2 TESTING TESTING 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

26/08/2025

Azimayi mukamaphika madzi osamba osamatelekela poto wa ndiwo. Abwanatu kuno angonunkhila ma Offals 😎

28/01/2025

MASIYA MANDA TO BULLETS???? LETS SEE WHY CHANCES ARE LOW

• Choyamba dziwana kuti atafika Peter Mponda ananena kuti samafuna squad yochuluka kwambiri mu team yake ndipo anapempha osewela ena achoke kuti atsale ndiosewela 25 basi.

• Bullets kwachoka osewela awa:
1. Shariff Sadick (to Reserve)
2. Sean McBrams (to Reserve)
3. Precious Sambani
4. Precious Phiri
5. Gomezgani Chirwa
6. Collin Mujuru
7. Nickson Nyasulu
8. Kesten Simbi
9. Ronald Chitiyo
10. Kenneth Pasuwa

• MAULLE ABWERETSA OSEWELA AWA:
1. Chikumbutso Henderson
2. Blessings Joseph
3. Andrew Jovinala

BULLETS SQUAD SO FAR

GOALKEEPERS
1. Clever Nkungula
2. Richard Chimbamba
3. Innocent Nyasulu

RIGHT BACK
1. Andrew Jovinala
2. Yamikani Mologeni

LEFT BACK
1. Alick Lungu
2. Crispin Mapemba

CENTRE BACK
1. Chikumbutso Henderson
2. Clyde Senaji
3. Blessings Joseph
4. Blessings Mpokera

DEFENDING MIDFIELDERS
1. Frank Willard
2. Yankho Singo

HOLDING MIDFIELDERA
1. Lloyd Aaron
2. Chawanangwa Gumbo
3. Wongani Lungu

ATTACKING MIDFIELDERS
1. Mike Mkwate
2. Enerst Petro

WINGERS
1. Peter Banda
2. Chikumbutso Salima
3. Lameck Gamphani

STRIKERS
1. Hassan Kajoke
2. Babatunde Adepoju
3. Ephraim Kondowe
4. Maxwell Gasten Phodo.

: Iyi ndi squad pakadali pano koma itha kuwonjezedwa osewela ena.

KODI BULLETS INGABWELETSESO RIGHT BACK?

• Yankho ndiloti ndizokaikitsa! Ma chances a Masiya Manda kupita ku Bullets ndiwochepa kwambiri.

• Bullets inkafuna Right Back mmodzi pakati pa Masiya Manda ndi Jovinala so kubwela kwa Jovinala kutimu yoti kuli kale Mologeni komaso Mpokera amasewera komweko nzosatheka.

• Panopa Bullets ngati ingabweletse Right Back ndie kuti ndiwaku Reserve, pakati pa Happy Mphepo kapena Andrew Lameck osatiso player wamkulu kale.

• MALO OMWE BULLETS INGAGULE OSEWELA ENA NDI ATI?
: Centre back mmodzi komaso Winger mmodzi, otherwise team ndiyamphavu zedi.

Nditsimikizeso kuti Hassan Kajoke, Mike Mkwate ndi Peter Banda omwe season yatha kunalibe akhale akubweletsa

Hello all membersNgati mukufuna ma cement concrete blocks contact or inbox me 0999 327 318And timapita pa plot yanu pomp...
26/01/2025

Hello all members

Ngati mukufuna ma cement concrete blocks contact or inbox me 0999 327 318

And timapita pa plot yanu pompo kuzakupangilani anu at a cheaper price

New model of toilet ❤️❤️❤️
20/01/2025

New model of toilet ❤️❤️❤️

Amazing toilet idea.

Address

Blantyre

Opening Hours

Monday 07:30 - 17:00
Tuesday 07:30 - 17:00
Wednesday 07:30 - 17:00
Thursday 07:30 - 17:00
Friday 07:30 - 17:00
Saturday 07:30 - 17:00

Telephone

+265999327318

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lloyd kanyimbi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Lloyd kanyimbi:

Share