Viphya Plantation Conservation Trust

Viphya Plantation Conservation Trust Seedlings and tree nursery available

put God first to succeed
19/06/2026

put God first to succeed

30/05/2026

Atsikana profile pic yomwe munali ku school mpaka pano muli ndi ana awiri osasintha? Hy, hello kapena hie akumapita kosayenera chonde.

Think of an Orchard...

30/05/2026

let's go wild

29/05/2026

😅😅😅

Ndinali okonda mowa ndipo tsiku lina mkazi wanga anandisekela pa khomo.
Ine kugogoda iye ati sindisegula ugona kunja komweko.

Mbali yakuseli kwanyumba yathu kunali zenje. Ndipo ndinamuopseza kuti Ukapanda kutsegula ndiziponya muzenje. Iye anandiyankha ha ha ha ha ziponyeni. Ulibe phindu lililonse iwe padziko pano.
😫

So ndinatenga chimwala chachikulu ndikuponya muzenje muja ndikubisala😅 mkazi anali ndi nkhawa amaganiza kuti ndaziponyadi. Mosakhalisa watsegula ndipo ine ndinalowa mwakachetechete ndikumutsekela😎😅

Kenako anagogoda. Ndipo Ndinamuuza kuti ugona kunja iwe😄
Ndipo anati Ukapanda kutsegula ndikuwa ndipo anthu abwera. Ndinamuuza kuti kuwani, ndipo anthu akabwela uzilongosola wekha kuti ukuchokela kuti nthawi ngat zino utangovala towel yokha🙌😅

14/03/2026

Address

Chikangawa

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Viphya Plantation Conservation Trust posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category