09/04/2026
Pamene tikupitilizabe kungwila ntchito yabwino malawi muno,pakuyika ma septic tank ya biodigester pamodzi ndi biogas.Tikudikila yinu kumeneko kuti nanunso mukhale nawo ma septic tank womwe : samafuna malo wochuluka kuti tiyike pa malo anu,samafunikila kupopetsa (samadzadza ),samamveka fungo loyipa,bwenzi la zachilengedwe.mutha kuyimba phone kapena whatsapp pa 0990642256 or tipezeni pa office yathu area 25C at B Complex Near FCB premises.