Hunters Technology Do it yourself -Diy

Hunters Technology Do it yourself -Diy Fixing broken/damaged electronic devices

Resistor colour coding..
28/12/2022

Resistor colour coding..

23/08/2022

*HuNTER TECH*

WE ARE EXPERTS IN FIXING

🪛 Laptops
🪛 Desktops
🪛 Phones
🪛 Home theater
🪛 Bluetooth speakers

WAP/CALL: 0994807010
*Appreciate our best services................................*

23/06/2022

Tili osangalala ukubweretserani makozedwe amafoni oyenela. Ngati foni yanu ili ndi vuto tiyankhuleni ku inbox kwathu ndipo muzayankhudwa pompo pompo ndi ma technician athu.
Tikuthandiza anthu kudzera pofoni p***a ngati ali ndi kuthekera kopanga okha koma akusowa kuti apanga bwanji. Ife tikuwawuza momwe ungapangire kuti athane ndi vuto la foni yawo mwa ukadaulo. Komaso tikuwauza kuti atipeze ku office yathu ku lilongwe kuti tiwakozere foni yawo.

Laptop yanu, nanga phone, screen, kapena chipangizo chinachilichose cha magetsi cha wonongeka munyumba mwanu, kuntchito ...
08/06/2022

Laptop yanu, nanga phone, screen, kapena chipangizo chinachilichose cha magetsi cha wonongeka munyumba mwanu, kuntchito kapena kulikose komwe muli.. tiyankhuleni ife a potumiza message pa send message button ili mmusiyi.. tikupezeka mu zomba ndi Lilongwe koma ngati sitingathe ukufikirani madera omwe anyamata athu sanakhazikikemo tikutha kupeleka ndondomeko yoti mutsate ngati mungakwanitse kukoza nokha chipangizo chanucho.

08/06/2022

We are offering high quality technical services at reasonable prices....
For more information hit our inbox or click on whatsapp button on this page..

07/06/2022

The important thing about a problem is not it's solution, but the strength we gain in finding the solution..

06/06/2022

We are pleased to bring to some of the computer software and hardware problems we are offering their solutions..
Power failure
Os Installation, recovery, activation and dual booting
Hinges
Data recovery

.

06/06/2022

Hunters Technology is so excited to announce that we are in Zomba and Lilongwe to help people with proper technical services. We have well trained technicians to provide you online as well as physical solutions to your gadgets...

03/06/2022

We offer online solutions of any electronic device. Just hit our inbox if you have a problem with your gadget. We will send you a solution of that particular fault only if you're will to do it by yourself otherwise we will direct you to where you will find us and fix that problem.

Address

Lilongwe

Telephone

+265994807010

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Hunters Technology Do it yourself -Diy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share