jmi energy

jmi energy energy

Cholera ndi matenda amene amayamba kapena kubwera chifukwa cha umve kapena kuti usi!! Izi zimachitika maka zowola zikach...
26/09/2022

Cholera ndi matenda amene amayamba kapena kubwera chifukwa cha umve kapena kuti usi!! Izi zimachitika maka zowola zikachuluka ndikusasamalidwa bwino kapenanso zimbudzi zosamangidwa bwino zitachuluka. Zimenezi zimayamba kupanga attract ntchencthe🪰🪰, kenako matendawa amayamba kufala. In my last training of biogas, I emphasized that human wastes, animal waste and any other rotten things", mmalo momadananazo can be converted into fortune (money) 💸💸💸. Human waste, animal waste and any other rotten wastes can bring us: 1.electricity
2. Cooking gas
3.Bio-fuel (methane)
Let's see opportunities in something that might look unwanted to us!! Sukulu imatiphunzitsa kuti zowola ndizoipa ine ndikuti zowola ndizabwino chifukwa zikhoza kutipangira ndalama ndikutichepetsera mavuto azachuma omwe dziko lathu likukumananawo!! KODI SITINGATHE KUMANGA MALAWI 🇲🇼 WAUKHONDO NDIWACHUMA POGWIRITSA NJIRA IMENEYI??

24/09/2022

Let's share the group

24/09/2022

By public demand I have created the page JMI ENERGY so that we reach one another on the aspect of innovation and development!!

Like the page and don't forget to share
Thanks

Address

Pretoria

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when jmi energy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category